Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 59
  • Tinadzipereka kwa Mulungu!

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tinadzipereka kwa Mulungu!
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tadzipereka kwa Mulungu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tadzipatulira kwa Mulungu!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Moyo Wopanda Mapeto—Potsiriza!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Lonjezo la Mulungu la Paradaiso
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 59

Nyimbo 59

Tinadzipereka kwa Mulungu!

Losindikizidwa

(Mateyu 16:24)

1. M’lungu wathu watikokera kwa Khristu

Kuti akhale m’busa wathu.

Cho’nadi tachipeza,

M’lungu wachibweretsa,

Ndipotu tadzikana,

Inde tikusangalala.

(KOLASI)

Ifetu tadzipereka kwa Yehova,

N’chifukwa chake tili okondwa.

2. M’pemphero tamulonjezatu Yehova

Kuti tidzamutumikira.

Tilidi okondwera

Moti tiuza ena,

Ufumu tilengeza

Dzina lake titchukitsa.

(KOLASI)

Ifetu tadzipereka kwa Yehova,

N’chifukwa chake tili okondwa.

(Onaninso Sal. 43:3; 107:22; Yoh. 6:44.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena