Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ssb nyimbo 211
  • Kugaŵana Mokondwa m’Kututa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kugaŵana Mokondwa m’Kututa
  • Imbirani Yehova Zitamando
  • Nkhani Yofanana
  • Tigwire Ntchito Yokolola Mosangalala
    Imbirani Yehova
  • Tizigwira Ntchito Yokolola Mosangalala
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Limbikirani ntchito yotuta!
    Nsanja ya Olonda—2001
  • M’minda Mwayera Kale Ndipo M’mofunika Kukolola
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Zitamando
Ssb nyimbo 211

Nyimbo 211

Kugaŵana Mokondwa m’Kututa

(Mateyu 9:37, 38)

1. Tiritu munthaŵi yotuta,

Mwaŵi wosayerekeza.

Angelowo ali “otuta,”

Ndipo tigaŵana nawo.

Yesu akuyambitsa zinthu,

Mwa kubzala mbewu ‘m’munda.’

Nthaŵi yakwana ya kututako;

Mokondwa tisonkhanitse.

2. ‘Tiriguyo’ ali mu “nkhokwe.”

“Namsongole” wasankhidwa.

Amene amasokoneza,

Akukuta mano awo.

Anthu a Yehova mu ntchito.

Mmaŵa kufika madzulo.

Kututa kwa nkhosa nkwakukulu,

Tisaleke kuthandiza.

3. Chikondi cha M’lungu ndi mnansi

Chisonkhezera ntchitoyo.

Ntchito iri yofulumira,

Chimaliziro chafika.

Kututa ndinthaŵi ya ntchito,

Kuthandiza ophunzira.

Chimwemwe cha tsiku ndi tsikudi,

Enanso azindikira.

4. Kristu Yesu ali kupenda

Kucha kwa dzinthu ziripo.

Mmene mmundamo ‘mwayerera!’

Ambiri aphunzitsidwe!

Chisangalalo nchachikulu,

Pogwira ntchito ndi M’lungu.

Mokondwera tikangalikebe;

Kwa iye ndi muntchitoyi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena