Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ssb nyimbo 47
  • Yehova, Nyonga Yathu ndi Mphamvu Yathu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova, Nyonga Yathu ndi Mphamvu Yathu
  • Imbirani Yehova Zitamando
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Ndi Mphamvu Yathu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Yehova Ndiye Mphamvu Yathu
    Imbirani Yehova
  • Ndipo Adzadziŵa
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Imvani Pemphero Langa
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Zitamando
Ssb nyimbo 47

Nyimbo 47

Yehova, Nyonga Yathu ndi Mphamvu Yathu

(Yesaya 12:2)

1. Yehova nyonga, ndi mphamvu yathu,

Mpulumutsi wathu, tikondwera.

Ndife mboni zanu za uthenga,

Kaya ’nthu amve pena akane.

(Korasi)

2. Mwa Kristu, timapeza mtendere;

Maso athu awona cho’nadi.

Ife timvatu lamulo lanu;

Kusankha kuima ndi Yehova.

(Korasi)

3. M’lungu tichita chifuno chanu.

Satana pokantha, tithemba’nu.

Nkana atiphe tithandizeni

Kukhala mboni zosunga ’mphumphu.

(KORASi)

Yehova Thanthwe ndi mphamvu yathu,

Tilengezabe Dzina lanu.

Yehova inu, Wamphamvuyonse,

Pobisala pathu; Nsanja yathu.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena