Nyimbo 208
Nyimbo ya Chikondwelero
1. Timva mphalasa.
Chisangalalo.
Mwana wa M’lungu alamula.
Nsanje zilira.
Nsalu ziŵala.
Mfu’yo imveka dziko lonse:
(Korasi)
2. Mwa kulalika
ndi kuphunzitsa,
Ambiri adza kwa Yehova.
Amaimbanso
Mosangalala,
Zikumamveka konsekonse!
(Korasi)
3. Tichitirane
Mwachikondidi
Anthu a Mulungu abale.
Kuimba kwathu
Kuwonje zebe
Chitamandocho kwa Yehova.
(KORASi)
Tsikuli ndi la Ya. (Idzani.)
Ufumu sudzatha. (Kondwa.)
Chinthu chiri chonse (Kondwani.)
Tamani M’lungu muimbe:
‘Kwa Ya tipeza chipulumutso
Ndi Kristu yemwe ali Mfumu.’