Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ssb nyimbo 75
  • Kutamanda Yehova Mokondwera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kutamanda Yehova Mokondwera
  • Imbirani Yehova Zitamando
  • Nkhani Yofanana
  • Kondwererani Chiyembekezo Chaufumu!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Kulemekeza Atate Wathu Yehova
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Gwirizanani Nawo m’Nyimbo Yaufumu!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Opatulidwa Kukhala Atamandi Achimwemwe pa Dziko Lonse
    Nsanja ya Olonda—1997
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Zitamando
Ssb nyimbo 75

Nyimbo 75

Kutamanda Yehova Mokondwera

(Salmo 63:5)

1. Ndi milomo yokondwera

Titamanda mwachimwemwe.

Yehova amagaŵira

Zonse zimene tifuna.

Ndi mitima yokondwera

Tifuula kwa Yehova.

Timamthokozadi nthaŵi zonse;

Moyo wathu ukondwera.

2. Anapereka Mwana’ke,

Akhale chipulumutso.

Timakweza manja athu,

Kupempherera chiyero.

Unansi wathu ulidi,

Monga chuma chapatali.

Chikondicho sichidzazirala;

Timkonda ndi moyo wonse.

3. Tiwona ulemerero.

Tikondwa ndi chitsogozo!

Mwachimwemwe timlambira,

Tidaliradi mwa iye.

Pansi pamapiko ake,

Tipezapo tchinjirizo!

Mtima uimba moyamikira;

Pakuti timamkondadi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena