Nyimbo 141
Mtundu Woyera wa Yehova
1. Padziko mtundu unabadwa
Kwa Yehovayo m’tsiku lathu.
Wavalitsidwa mwachiyero,
Ulambira motheratu.
(Korasi)
2. Mokondwa mtundu woyerawu
Ulengeza dzina la M’lungu.
Monga chizindikiro chawo
Amalengeza Ufumu.
(Korasi)
3. Mtundu wa Yehova Ngwokondwa
Nkhosa zina ziima nawo.
Amatumikira pamodzi
Akhala m’chiyanjo cha Ya.
(KORASi)
Nkokwezekadi, sikungaime,
Kulambirako m’Ziyoni.
Mtundu wake ndi ‘khamulo’
Amasangalatsa Yehova.