Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 17
  • Pitani Patsogolo Mboninu!

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pitani Patsogolo Mboninu!
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Pitani Patsogolo Mboninu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tiyeni, Mboninu!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Pitani Patsogolo, Inu Atumiki a Ufumu!
    Imbirani Yehova
  • Pitirizani Kulalikira za Ufumu
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 17

Nyimbo 17

Pitani Patsogolo Mboninu!

Losindikizidwa

(Luka 16:16)

1. Olimba m’nthawi yamapeto ino,

Ndife oteteza uthenga wabwino.

Satana ’ngatsutse koopsa,

Mumphamvu ya Mulungu sitigonja.

(KOLASI)

Ndiye pitani patsogolo Mboninu!

Kondwerani pogwira ntchito ya M’lungu!

Uzani onse zadziko latsopano

Momwe mudzakhala madalitso.

2. Tisatengeke ndi moyo wofewa,

Kusangalatsa dzikoli tizipewa.

Mawanga a dziko tikane

Ndi kukhala okhulupirikabe.

(KOLASI)

Ndiye pitani patsogolo Mboninu!

Kondwerani pogwira ntchito ya M’lungu!

Uzani onse zadziko latsopano

Momwe mudzakhala madalitso.

3. Ufumu wa M’lungu ukunyozedwa,

Dzina lake loyera likudetsedwa.

Tiyenitu tiliyeretse,

Kumitundu yonse tililengeze.

(KOLASI)

Ndiye pitani patsogolo Mboninu!

Kondwerani pogwira ntchito ya M’lungu!

Uzani onse zadziko latsopano

Momwe mudzakhala madalitso.

(Onaninso Afil. 1:7; 2 Tim. 2:3, 4; Yak. 1:27.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena