Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 52
  • Tetezani Mtima Wanu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tetezani Mtima Wanu
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Titeteze Mtima Wathu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Khalani ndi Mtima Wovomerezeka kwa Yehova
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Kuwafika Pamtima Omvetsera Anu
    Buku Lolangiza la Sukulu ya Utumiki Wateokalase
  • Pitirizani Kutumikira Yehova ndi Mtima Wathunthu
    Nsanja ya Olonda—2012
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 52

Nyimbo 52

Tetezani Mtima Wanu

Losindikizidwa

(Miyambo 4:23)

1. Tetezani mtima wanu

Mukhale ndi moyo.

Mulungu adziwa bwino

Mmene tililidi.

Mtima ndi wonyenga

ungakusocheretseni.

Choncho ganizani bwino,

Mverani Yehova.

2. Konzanitu mtima wanu

Ufune Yehova

Pempherani muuzeni

Za kukhosi kwanu.

Zomwe M’lungu aphunzitsa

Tiyeni timvere,

Choncho tidzamutamanda

Tsiku lililonse.

3. Tetezani mtima wanu

Mupewe zoipa.

Akufikeni pa mtima.

Mawu a Mulungu

Yehova akonda onse

Okhulupirika.

Choncho mulambirenitu

Monga bwenzi lake.

(Onaninso Sal. 34:1; Afil. 4:8; 1 Pet. 3:4.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena