Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 99
  • Tamandani Mfumu Yatsopano ya Dziko Lapansi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tamandani Mfumu Yatsopano ya Dziko Lapansi
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Tamandani Mfumu Yatsopano Yolamulira Dziko Lapansi
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Chimwemwe Chosatha
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!
    Imbirani Yehova
  • Tamandani Yehova Mulungu Wathu
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 99

Nyimbuo 99

Tamandani Mfumu Yatsopano ya Dziko Lapansi

Losindikizidwa

(Chivumbulutso 7:9)

1. Khamu lalikulu

Lochokera m’mitundu yonse

Likusonkhanitsidwa ndi Khristu

ndi mpingo wake.

Ufumu wabadwa

ndipo udzalamulira dziko.

Chiyembekezochi ndi mphatso

Yotisangalatsa tonse.

(KOLASI)

Tamandani M’lungu,

Tamandani Yesu

Omwe anatipulumutsa.

Tsopano tingayembekezere

Kukhala kwamuyaya.

2. Tikutamanda Khristu Mfumu

poimba mokondwa.

Iyetu adzachita

chifuniro cha Yehova.

Tikuonadi m’tsogolo

mulidi chisangalalo,

Akufa tidzawaonanso,

Zonse zomwe timakonda!

(KOLASI)

Tamandani M’lungu,

Tamandani Yesu

Omwe anatipulumutsa.

Tsopano tingayembekezere

Kukhala kwamuyaya.

(Onaninso Sal. 2:6; 45:1; Yes. 9:6; Yoh. 6:40.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena