Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 92
  • “Lalikira Mawu”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Lalikira Mawu”
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • “Lalikira Mawu”
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • “Lalika Mawu”!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Tilalikire Mbiri Yabwino Imeneyi Yaufumu
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Ndi Ndani Amene Amalalikira Uthenga Wabwino?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 92

Nyimbo 92

“Lalikira Mawu”

Losindikizidwa

(2 Timoteyo 4:2)

1. Mulungu watilamula,

Ndipo tikufunika kumvera.

Tifotokozeretu anthu

Adziwe chiyembekezo chathu.

(KOLASI)

Lalikira,

Indetu onse amve!

Lalika

Dzikoli lisanathe.

Lalika,

Ofatsa amvetsetse.

Lalika

M’dziko lonse.

2. Mavuto adzatiyesa.

Tingapezeke tikunyozedwa,

N’kulowa m’mavuto a’kulu.

Tidzakhulupirirabe M’lungu.

(KOLASI)

Lalikira,

Indetu onse amve!

Lalika

Dzikoli lisanathe.

Lalika,

Ofatsa amvetsetse.

Lalika

M’dziko lonse.

3. Nthawi ina tidzapeza

Anthu ofunadi kumvetsera.

Tiwaphunzitsa ’pulumuke,

Dzina la Yehova tiyeretse.

(KOLASI)

Lalikira,

Indetu onse amve!

Lalika

Dzikoli lisanathe.

Lalika,

Ofatsa amvetsetse.

Lalika

M’dziko lonse.

(Onaninso Mat. 10:7; 24:14; Mac. 10:42; 1 Pet. 3:15.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena