Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 56
  • Mulungu Imvani Pemphero Langa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mulungu Imvani Pemphero Langa
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Imvani Pemphero Langa
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Yehova, Nyonga Yathu ndi Mphamvu Yathu
    Imbirani Yehova Zitamando
  • M’patseni Yehova Ulemerero
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nyimbo kwa Wammwambamwambayo
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 56

Nyimbo 56

Mulungu Imvani Pemphero Langa

Losindikizidwa

(Salimo 54)

1. Tate wanga chonde ndimveni

M’lungu wanga ine ndi wanu.

Dzina lanu ndi lalikulu

(KOLASI)

Yehova ’Tate ndimvereni.

2. Ndathokoza ndadzuka bwino.

Mwandipatsa mphatso ya moyo.

Mumandisangalatsa mtima.

(KOLASI)

Yehova ’Tate ndimvereni.

3. Ndikufunitsitsa kuchita

Zoyenera. Mundithandize

Ndipirire mavuto onse.

(KOLASI)

Yehova ’Tate ndimvereni.

(Onaninso Eks. 22:27; Sal. 106:4; Yak. 5:11.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena