Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsamba 6
  • Muzitsanzira Yesu Pokana Mayesero

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzitsanzira Yesu Pokana Mayesero
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Ganizirani za Mtundu wa Munthu Amene Muyenera Kukhala
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Muzikonda Chilungamo Ndipo Muzidana ndi Kusamvera Malamulo
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Kodi Ndingatani Kuti Ndisamagonje Poyesedwa?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 June tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 4-5

Muzitsanzira Yesu Pokana Mayesero

Satana amafuna kuwononga ubwenzi wathu ndi Yehova pogwiritsa ntchito zimene mtima wathu umalakalaka. Iye amayesa munthu aliyense mogwirizana ndi zimene amalakalaka komanso zomwe zikuchitika pa moyo wake.

Kodi Yesu anagwiritsa ntchito chiyani pokana mayesero atatu amene Satana amagwiritsa ntchito kwambiri? (Aheb. 4:12; 1 Yoh. 2:15, 16) Nanga kodi ndingamutsanzire bwanji?

  • Yesu akukana kusandutsa miyala kuti ikhale mikate

    4:1-4

    “Chilakolako cha thupi”

  • Yesu akukana kugwadira Satana atamuuza kuti amupatsa maufumu onse a dziko lapansi

    4:5-8

    “Chilakolako cha maso”

  • Yesu ali pamwamba pa khoma la mpanda wa kachisi

    4:9-12

    “Kudzionetsera”

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena