June 25–July 1
Luka 4-5
Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzitsanzira Yesu Pokana Mayesero”: (10 min.)
Luka 4:1-4—Yesu sanalole kuti chilakolako cha thupi chimugonjetse (w13 8/15 25 ¶8)
Luka 4:5-8—Yesu sanakopeke ndi chilakolako cha maso (w13 8/15 25 ¶10)
Luka 4:9-12—Yesu sanagonje pamene anayesedwa kuti achite zinthu modzionetsera [Onerani vidiyo yakuti Pamwamba pa Khoma la Mpanda wa Kachisi.] (“Pamwamba pa Khoma la Mpanda wa Kachisi” zithunzi ndi mavidiyo pa Luka 4:9, nwtsty; w13 8/15 26 ¶12)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Luka 4:17—Kodi n’chiyani chikusonyeza kuti Yesu ankadziwa bwino Mawu a Mulungu? (“mpukutu wa mneneri Yesaya” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 4:17, nwtsty)
Luka 4:25—Kodi chilala chimene chinachitika m’nthawi ya Eliya chinatenga nthawi yaitali bwanji? (“zaka zitatu ndi miyezi 6” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 4:25, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 4:31-44
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako musiyireni khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG.
Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl mutu 28
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzisamala Mukamacheza ndi Anzanu pa Intaneti”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzichita Zinthu Mwanzeru Mukamacheza ndi Anzanu pa Intaneti.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 20 ¶17-19 komanso tsamba 216, 217, 218-219
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero