Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 December tsamba 7
  • “Mukhale Tcheru ndi Kuyang’anira Gulu Lonse la Nkhosa”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Mukhale Tcheru ndi Kuyang’anira Gulu Lonse la Nkhosa”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • “Wetani Gulu la Nkhosa za Mulungu Lomwe Analisiya M’manja Mwanu”
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Abusa, Tsanzirani Abusa Aakulu
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Musawopa, Kagulu ka Nkhosa Inu”
    Nsanja ya Olonda—1995
  • Thandizani Osochera Kubwerera M’gulu la Nkhosa
    Nsanja ya Olonda—2008
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 December tsamba 7
Akulu akucheza ndi ena ku Nyumba ya Ufumu

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 19-20

“Mukhale Tcheru ndi Kuyang’anira Gulu Lonse la Nkhosa”

20:28, 31, 35

Mkulu akulankhula ndi dokotala pamene m’bale wagonekedwa m’chipatala

Akulu amadyetsa, kuteteza ndi kusamalira nkhosa chifukwa amadziwa kuti nkhosazo zinagulidwa ndi magazi a mtengo wapatali a Yesu. Abale ndi alongo amayamikira kwambiri akulu omwe ali ngati Paulo, amene amadzipereka posamalira nkhosa.

Dzifunseni kuti, ‘Kodi ineyo ndimasonyeza bwanji kuyamikira ntchito yaikulu imene akulu amagwira mumpingo?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena