Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 March tsamba 2
  • Mmene Tingasonyezere Chikondi Chachikhristu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mmene Tingasonyezere Chikondi Chachikhristu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Chikondi cha Mulungu N’chosatha
    Imbirani Yehova
  • Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • “Musabwezere Choipa pa Choipa”
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
    Galamukani!—2022
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 March tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 12-14

Mmene Tingasonyezere Chikondi Chachikhristu

12:10, 17-21

Munthu wina akatilakwira sitimangofunika kupewa kumuchitira zoipa. Koma ngati tili ndi chikondi chachikhristu, tidzamuchitirabe zinthu mokoma mtima. Baibulo limati: “Ngati mdani wako ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse chakumwa. Pakuti mwa kutero udzamuunjikira makala a moto pamutu pake.” (Aroma 12:20) Zinthu zabwino zimene tingachitire munthu amene watilakwira zingathandize kuti munthuyo adzimvere chisoni n’kusintha.

Mlongo wachitidwa chipongwe ndi mnzake wakuntchito ndipo madzulo a tsikulo akuuza mkulu wina zomwe zachitika. Tsiku lotsatira akuchita zinthu mokoma mtima ndi mnzake wakuntchito uja

Kodi munamva bwanji pamene munthu wina yemwe munamulakwira mosadziwa anakuchitirani zinthu mokoma mtima?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena