Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 114
  • “Khalani Oleza Mtima”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Khalani Oleza Mtima”
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Kuleza Mtima
    Imbirani Yehova
  • Tsanzirani Kuleza Mtima kwa Yehova
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Kuleza Mtima N’kofunika Kwambiri pa Utumiki Wathu
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
  • Kodi Mungatani Kuti Mukhale Woleza Mtima?
    Mfundo Zothandiza Mabanja
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 114

NYIMBO 114

“Khalani Oleza Mtima”

Losindikizidwa

(Yakobo 5:8)

  1. 1. Yehova M’lungu wathu,

    Dzina lake ndi loyera.

    Amafunitsitsatu

    Kuliyeretsa dzinali.

    Wakhala wopirira

    Kwa nthawi yaitali.

    Amalezanso mtima

    Ndipo samatopa.

    Cholinga chake n’choti

    Anthu adzapulumuke.

    Adzapitirizabe

    Kukhala oleza mtima.

  2. 2. Tikamaleza mtima

    Timamvera M’lungu wathu.

    Ndi khalidwe labwino,

    Timatha kupewa mkwiyo,

    Timaona zabwino

    Mwa ena nthawi zonse,

    Limatithandizanso

    Tikamavutika.

    Makhalidwe amene

    Timapatsidwa ndi mzimu

    Amatithandizadi

    Kutsanzira M’lungu wathu.

(Onaninso Eks. 34:14; Yes. 40:28; 1 Akor. 13:​4, 7; 1 Tim. 2:4.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena