Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • scl tsamba 34
  • Kudzikayikira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kudzikayikira
  • Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
scl tsamba 34

Kudzikayikira

Kodi n’chiyani chingachitike tikamadzikayikira komanso kudziona ngati osafunika pamaso pa Yehova?

Nu 11:14, 15; 1Mf 19:1-4; Yob 3:3; Yer 15:10

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Da 10:8-11, 18, 19​—Mneneri Danieli ankadzikayikira koma analimbikitsidwa mngelo atamukumbutsa kuti ndi wofunika kwambiri kwa Yehova

    • Mt 10:29-31​—Yesu ananena fanizo la mpheta pofuna kutisonyeza kuti Yehova amatikonda komanso amatisamalira

  • Malemba otonthoza:

    • Yer 31:3; Yoh 6:44; Ahe 6:10; 1Pe 1:18, 19; 1Yo 3:19, 20

    • Onaninso Sl 56:8; Yer 29:11

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena