Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mrt nkhani 5
  • Njira Zothandiza Powerenga Baibulo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Njira Zothandiza Powerenga Baibulo
  • Nkhani Zina
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ndingatani Kuti Kuŵerenga Baibulo Kuzindisangalatsa?
    Galamukani!—2001
  • Kubwereza Gawo 1
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Mmene Banja Limachitira Zinthu Kuti Onse Azitengamo Mbali Mokwanira—Pa Phunziro la Baibulo
    Utumiki Wathu wa Ufumu—1999
  • Sukulu ya Utumiki Wateokalase ya 2002
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2001
Onani Zambiri
Nkhani Zina
mrt nkhani 5
Mzimayi akuyang’ana ndandanda yowerengera Baibulo ya pa jw.org

Njira Zothandiza Powerenga Baibulo

Baibulo lili ndi mfundo zothandiza kwambiri. Mukamaliwerenga ndi kuganizira mwakuya zimene mwawerengazo, komanso kugwiritsa ntchito zomwe mwaphunzirazo, mudzakhala “ndi moyo wopambana.” (Yoswa 1:8; Salimo 1:1-3) Mudzamudziwanso bwino Mulungu ndi Mwana wake Yesu ndipo zimenezi zingakuthandizeni kuti mudzapulumuke.​—Yohane 17:3.

Ndandanda Yowerengera Baibulo

Kodi mungakonde kutsatira ndondomeko iti powerenga Baibulo? Pamenepatu mungasankhe. Ndandanda yowerengera Baibuloyi ikuthandizani kuti muwerenge Baibulo potsatira ndondomeko ya mmene mabuku ake alili kapena potsatira nkhani zomwe mwasankha. Mwachitsanzo, mutha kuwerenga nkhani zokuthandizani kukhala ndi chithunzi cha mmene Mulungu ankachitira zinthu ndi Aisiraeli. Mutha kuwerenga mbali zina za Baibulo kuti mudziwe mmene mpingo wachikhristu unayambira komanso mmene unakulira. Mukamawerenga machaputala omwe agawidwa kalewo tsiku lililonse, mutha kumaliza kuwerenga Baibulo lonse chaka chimodzi.

Ndandandayi ingakuthandizeni kwambiri kaya mukufuna kumangowerenga Baibulo tsiku lililonse, kukhala ndi cholinga chomaliza kuwerenga Baibulo chaka chimodzi kapena kutsatira ndondomeko yowerengera Baibulo ya anthu omwe angoyamba kumene. Pangani dawunilodi ndandanda yowerengera Baibulo, ndipo yambani lero.

Pangani dawunilodi

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena