Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • yp2 tsamba 112-113
  • Moyo wa Kusukulu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Moyo wa Kusukulu
  • Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
  • Nkhani Yofanana
  • Mfundo Zanga—Moyo wa Kusukulu
    Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
  • Mmene Mungalangizire Ana Anu
    Mfundo Zothandiza Mabanja
  • Kodi Ndisiye Sukulu?
    Galamukani!—2010
  • Sukulu Yopambana Yapadziko Lonse
    Galamukani!—1996
Onani Zambiri
Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
yp2 tsamba 112-113

Chigawo 4

Moyo wa Kusukulu

Kodi pali maphunziro ena amene amakuvutani kwambiri?

□ Inde

□ Ayi

Kodi munayamba mwavutitsidwapo kapena kuchitiridwa zachipongwe ndi anzanu a kusukulu?

□ Inde

□ Ayi

Kodi nthawi zina mumatengeka ndi makhalidwe a anzanu a kusukulu?

□ Inde

□ Ayi

Mwina mungaganize kuti: ‘Ngati nditakwanitsa kumaliza sukulu bwinobwino ndiye kuti palibenso china chilichonse chimene chingandivute.’ Zimenezi zikhoza kukhala zoona chifukwa kusukulu n’kumene kumavuta kwambiri kuti munthu asonyeze kuti ndi wanzeru, wosakwiya msanga ndiponso wokonda Mulungu. Kodi mungatani kuti muphunzire bwinobwino popanda kutengera makhalidwe oipa a anzanu a kusukulu? Mitu 13 mpaka 17 ikuthandizani kwambiri pankhani zimenezi.

[Chithunzi chachikulu pamasamba 112, 113]

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena