Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 74
  • Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka”
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Chimwemwe cha Yehova Ndicho Linga Lathu
    Nsanja ya Olonda—1995
  • Nyimbo Yatsopano
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nyimbo Yatsopano
    Imbirani Yehova
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 74

Nyimbo 74

Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka

Losindikizidwa

(Nehemiya 8:10)

1. Zizindikiro za nthawi inoyi

Zikulengeza ufumu.

Chipulumutsotu chayandikira

Tukulani mitu yanu.

(KOLASI)

Chimwemwe chomwe Yehova ’patsa

Ndi malo achitetezo.

Imbani mofuula ndi chimwemwe,

Khalani ndi chiyembekezo.

Chimwemwe chomwe Yehova ’patsa

Ndi malo achitetezo.

Modzipereka tidzamulambira.

Mwachimwemwe tim’tumikira.

2. Inu amene mukonda Yehova,

Mudalireni ngwamphamvu.

Imirirani ndipo fuulani,

Imbani mokweza mawu.

(KOLASI)

Chimwemwe chomwe Yehova ’patsa

Ndi malo achitetezo.

Imbani mofuula ndi chimwemwe,

Khalani ndi chiyembekezo.

Chimwemwe chomwe Yehova ’patsa

Ndi malo achitetezo.

Modzipereka tidzamulambira.

Mwachimwemwe tim’tumikira.

(Onaninso 1 Mbiri 16:27; Sal. 112:4; Luka 21:28; Yoh. 8:32.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena