Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 4/12 tsamba 3
  • Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
km 4/12 tsamba 3

Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu

Mafunso otsatirawa tidzawakambirana pa Sukulu ya Utumiki wa Mulungu ya mlungu woyambira April 30, 2012. Taika tsiku limene likusonyeza mlungu umene mfundoyo idzakambidwe n’cholinga choti muthe kufufuza pamene mukukonzekera sukulu mlungu uliwonse.

1. N’chifukwa chiyani buku la Yeremiya ndi lothandiza kwa ifeyo? [Mar. 5, w11 3/15 tsa. 29 ndime 4–tsa. 30 ndime 11; si-E tsa. 129 ndime 36]

2. Kodi Yehova angatilanditse bwanji ku chizunzo masiku ano? (Yer. 1:8) [Mar. 5, w05 12/15 tsa. 23 ndime 18; w07 3/15 tsa. 9 ndime 7]

3. Kodi odzozedwa anabwerera liti ndiponso motani ku “njira zakale”? (Yer. 6:16) [Mar. 12, w05 11/1 tsa. 24 ndime 12]

4. N’chifukwa chiyani tinganene kuti masiku ano mu ‘Giliyadi muli basamu’? (Yer. 8:22) [Mar. 19, w10 6/1 tsa 22 ndime 3–tsa. 23 ndime 4]

5. Kodi tingalimbane bwanji ndi zinthu zofooketsa zimene timakumana nazo nthawi ndi nthawi? (Yer. 15:16, 17) [Mar. 26, w07 3/15 tsa. 10 ndime 3]

6. Kodi Yehova “anadabwitsa” bwanji Yeremiya ndipo ifeyo tikuphunzirapo chiyani? (Yer. 20:7) [Apr. 2, w07 3/15 tsa. 9 ndime 6; jr-E tsa. 36 ndime 8]

7. Kodi mavesi amenewa amatiphunzitsa chiyani za Yehova? (Yer. 21:8, 9) [Apr. 2, w07 3/15 tsa. 11 ndime 6]

8. N’chifukwa chiyani “uthenga wa Yehova” unali katundu wolemetsa? (Yer. 23:33) [Apr. 9, w07 3/15 tsa. 11 ndime 1]

9. Kodi chilamulo cha Mulungu chimalembedwa motani m’mitima? (Yer. 31:33) [Apr. 23, w07 3/15 tsa. 11 ndime 2]

10. Kodi cholinga chomwe ankalembera zikalata ziwiri zokhudza pangano limodzi chinali chiyani? (Yer. 32:10-15) [Apr. 30, w07 3/15 tsa. 11 ndime 3]

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena