Anthu Okonda Mtendele
M’maŵa
08:40 Nyimbo Zamalimba
08:50 Nyimbo Na. 58 na Pemphelo
09:00 Takulandilani, Anthu Okonda Mtendele!
09:15 Pitilizani Kufuna-funa Anthu Okonda Mtendele
09:30 Lolani Kalonga Wamtendele Kukuthandizani Kupeza Anthu Okonda Mtendele
09:55 Nyimbo Na. 103 na Zilengezo
10:05 Anthu Okonda Mtendele Saphunzilanso Nkhondo
10:35 Kudzipatulila na Ubatizo
11:05 Nyimbo Na. 79
Masana
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 76
12:35 Zocitika
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Yosiyilana: Anthu Okonda Mtendele Amathandizana
• “Futukulani Mtima Wanu”
• Thandizani Anthu Acicepele Kupita Patsogolo Kuuzimu
• Lemekezani Okalamba
14:00 Nyimbo Na. 57 na Zilengezo
14:10 Mmene Anthu Okonda Mtendele Amagonjetsela Coipa mwa Kucita Cabwino
14:55 Nyimbo Na. 45 na Pemphelo