Zamkati
February 1, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI ZOPHUNZILA
APRIL 7-13, 2014
Tamandani Kristu, Mfumu Yaulemelelo!
TSAMBA 8 • NYIMBO: 99, 107
APRIL 14-20, 2014
Sangalalani Cifukwa ca Cikwati ca Mwanawankhosa
TSAMBA 13 • NYIMBO: 109, 100
APRIL 21-27, 2014
Yehova Amatisamalila ndi Kutiteteza
TSAMBA 18 • NYIMBO: 60, 51
APRIL 28, 2014–MAY 4, 2014
Yehova Ndi Bwenzi Lathu Lapamtima
TSAMBA 23 • NYIMBO: 91, 63
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Tamandani Kristu, Mfumu Yaulemelelo!
▪ Sangalalani Cifukwa ca Cikwati ca Mwanawankhosa
Monga Mfumu Mesiya, Yesu Kristu wamangilila lupanga m’ciuno mwake ndipo akupita kukagonjetsa adani ake. Akadzamaliza kuwagonjetsa, iye adzakwatila mkazi wokongola ndipo anamwali anzake adzasangalala pamodzi ndi mkaziyo. Lemba la Salimo 45 limafotokoza zocitika zocititsa cidwi zimenezi. Tidzaphunzila mmene zocitikazi zimatikhuzila.
▪ Yehova Amatisamalila ndi Kutiteteza
▪ Yehova Ndi Bwenzi Lathu Lapamtima
Kodi tingalimbitse bwanji ubwenzi wathu ndi Atate wathu wakumwamba? Nkhani zimenezi zidzatithandiza kulimbitsa ubwenzi wathu ndi Yehova amene ndi Mpatsi wathu, Mtetezi wathu ndi Bwenzi lathu lapamtima. Zidzatilimbikitsanso kuthandiza ena kumulemekeza.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
3 Nkhondo Imene Inasintha Zinthu Padziko
5 Kodi Ndani Maka-maka Amacititsa Nkhondo ndi Mavuto?
28 Tsanzilani Cikhulupililo Cao—Anapilila Zinthu Zopanda Cilungamo