Ndandanda ya Mlungu wa January 28
MLUNGU WA JANUARY 28
Nyimbo 29 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 18 ndime 6-11 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Mateyu 16-21 (Mph. 10)
Na. 1: Matthew 17:22–18:10 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi ndi ‘Mau Abwino’ Ati a Yehova Amene Yoswa Anaona Akukwanilitsidwa?—Yos. 23:14 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi ndi Maulosi Ena Ati Apadela a m’Baibo Amene Sanakwanilitsidwebe?—rs tsa. 389 ndime 2–tsa. 390 ndime 2 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 134
Mph. 5: Yambitsani Phunzilo la Baibo pa Ciŵelu Coyamba. Mwa kugwilitsila nchito ulaliki wacitsanzo uli patsamba 4, onetsani mmene tingayambitsile phunzilo pa Ciŵelu coyamba mu February. Limbikitsani onse kutengako mbali.
Mph. 10: “Mmene Tingathetsele Kaduka.” Nkhani yocekela mu Nsanja ya Olonda ya February 15, 2012 tsa. 16 ndime 7 mpaka tsa. 17 ndime 3.
Mph. 15: “Cikondi ca Kristu Cimatilimbikitsa Kukonda Ena.” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo 53 ndi Pemphelo