Ndandanda ya Mlungu wa September 23
MLUNGU WA SEPTEMBER 23
Nyimbo 109 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
jl phunzilo 3 mpaka 4 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: 2 Akorinto 8-13 (Mph. 10)
Na. 1: 2 Akorinto 10:1-18 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Ngati Wina Wanena Kuti, ‘Ndimakhulupilila Kuti Munthu Akafa Amakabadwanso Kwinakwake’—(rs tsa. 178 ndime 2-4) (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Lemba la 1 Akorinto 10:13 Limatanthauza Ciani? (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 43
Mph. 5: “Ndidzatenga Mabuku Anu Mukatenga Anga.” Kukambitsilana. Pemphani omvela kuti afotokoze mmene agwilitsilila nchito malingalilo amenewa. Citani citsanzo cacidule.
Mph. 25: “Njila Zatsopano Zocitila Ulaliki Wapoyela.” Mafunso ndi mayankho. Fotokozani makonzedwe alionse amene mpingo wanu wapanga ocita ulaliki wapoyela mwa kugwilitsila nchito mathebulo kapena mashelufu a mawilo oikapo magazini ndi mabuku. Fotokozani kuti Mboni si ziyenela kutenga mabuku kapena magazini pa malo amenewa.
Nyimbo 44 ndi Pemphelo