Ndandanda ya Mlungu wa March 31
MLUNGU WA MARCH 31
Nyimbo 105 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 6 ¶13-18 ndi bokosi patsamba 74 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Ekisodo 1-6 (Mph. 10)
Na. 1: Ekisodo 2:1-14 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kubwelanso kwa Kristu Kudzakhala Kosaoneka—rs tsa. 162 ndime 3 mpaka tsa. 163 ndime 1 (Mph. 5)
Na. 3: Kutsutsana ndi Anthu Osankhidwa Ndi Mulungu Kuli Ngati Kutsutsana ndi Yehova—lv-tsa 43 mpaka tsa. 44 ndime 15-17 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 63
Mph. 10: “Gwilitsilani Nchito Bwino Magazini Akale.” Nkhani yokambitsilana. Lengezani ngati mpingo uli ndi magazini akale amene ofalitsa angagwilitsile nchito mu ulaliki. Pemphani omvela kuti afotokoze zocitika zimene anapeza pogwilitsila nchito magazini akale. Kumapeto a nkhani, pemphani woyang’anila nchito kuti afotokoze mmene nchito yogaŵila tumapepala toitanila anthu ku Cikumbutso ikuyendela.
Mph. 10: Zosoŵa za pampingo.
Mph. 10: Kodi Tiphunzilapo Ciani? Nkhani yokambitsilana. Malemba awa aŵelengedwe Mateyu 28:20 ndi 2 Timoteyo 4:17. Kambitsilanani mmene malemba amenewa angatithandizile mu ulaliki.
Nyimbo 135 ndi Pemphelo