LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 12/14 tsa. 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa December 15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa December 15
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Tumitu
  • MLUNGU WA DECEMBER 15
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 12/14 tsa. 2

Ndandanda ya Mlungu wa December 15

MLUNGU WA DECEMBER 15

Nyimbo 1 ndi Pemphelo

Phunzilo la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 2 ndime 12 mpaka 20 (Mph. 30)

Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibulo: Yoswa 6-8 (Mph. 10)

Na. 1: Yoswa 8:18-29 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

Na. 2: N’ciani Cimatsimikizila Kuti Munthu Ali ndi Mzimu Woyela?—rs tsa. 320 ndime 3–tsa. 321 ndime 2 (Mph. 5)

Na. 3: N’cifukwa Ciani Satana Mdyelekezi ndi Mdani Wathu Wamkulu?—rs tsa. 352 (Mph. 5)

Msonkhano wa Nchito:

Lemba la Mwezi: Tulutsani “zabwino” m’cuma cabwino cimene mwapatsidwa.—Mat. 12:35a.

Nyimbo 101

Mph. 15: “Kucititsa Maphunzilo a Baibulo Mogwila Mtima.” Mafunso ndi mayankho. Mukakambilana ndime 3, mucite citsanzo ca mbali ziŵili coonetsa wofalitsa akukambilana ndi wophunzila Baibulo m’ndime 8 ya nkhani 15 m’buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa. Citsanzo coyamba, cionetse wofalitsa akulankhula kwambili. Koma caciŵili cionetse wofalitsa akufunsa mafunso ofuna kuti wophunzila anenepo maganizo ake n’colinga coti adziŵe maganizo a wophunzilayo.

Mph. 15: Cida Cokuthandizani Kukonzekela Kucititsa Maphunzilo a Baibulo. Kukambilana. Thandizani omvela kuona mbali ya pa jw.org pa mutu wakuti, “Kodi Baibulo Limaphunzitsa Ciani?” (Onani polemba kuti, BIBLE TEACHINGS > TEENAGERS.) Kambilanani mmene nkhani imeneyi ingagwilitsidwile nchito ndi colinga coti ticititse maphunzilo a Baibulo mogwila mtima kwa ana ndi acikulile. Kodi mafunso amene ali pa zithunzi zimenezi, angatithandize bwanji kuwafika pa mtima ophunzila? Phatikizanipo citsanzo coonetsa wofalitsa akulankhula yekha. Iye akugwilitsila nchito cithunzi cimodzi pamene akuganizila zosowa za wophunzila wake ndiyeno akukonzekela mafunso ogwila mtima. Malizani mwa kulimbikitsa onse kukhala aphunzitsi aluso mwa kuyesetsa kuwafika pa mtima ophunzila ao ndi kugwilitsila nchito zinthu zabwino zimene tili nazo pothandiza ena. (Miy. 20:5) Ngati mulibe Intaneti, kambilanani nkhani yakuti, “Konzekerani Bwino Pokaphunzitsa,” yopezeka patsamba 2 mu Utumiki Wathu wa Ufumu wa June 2009.

Nyimbo 99 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani