Ndandanda ya Mlungu wa March 2
MLUNGU WA MARCH 2
Nyimbo 5 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu. 6 ndime 1-8 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Rute 1-4
Na. 1: Rute 3:14–4:6 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Akula —Mutu: Muzilalikila Mwacangu Ndiponso Khalani Woceleza—w111/15 tsa. 14-15 ndime 11,12 (Mph. 5)
Na. 3: Kudzicepetsa Ndiponso Mphamvu za Kristu Mfumu—igw-CIN tsa. 8 ndime 5–tsa. 9 ndime 1–4 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: Khalani “Odzipeleka pa Nchito Zabwino.”—Tito 2:14.
Nyimbo 121
Mph. 10: Kugaŵila Magazini mu March. Kukambilana. Yambani mwa kucita citsanzo coonetsa mmene tingagaŵile magazini pogwilitsila nchito maulaliki a zitsanzo ali patsamba lino. Limbikitsani onse kuŵadziŵa bwino magazini athu.
Mph. 10: “Muzilimbikitsana pa Nchito Zabwino Modzipeleka.” Kukambilana. Fotokozani mmene lemba la mwezi linagogomezedwela pa misonkhano ya nchito mu February.
Mph. 10: Tinacita Zotani? Kukambilana. Pemphani omvela kuti afotokoze ubwino umene apeza pogwilitsila nchito mfundo za m’nkhani yakuti “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Ulaliki Wapoyela M’gawo la Mpingo Wanu.” Ngati ndi kotheka, funsani ofalitsa kuti akambe cimene cinawathandiza pocita ulaliki wapoyela.
Nyimbo yatsopano “Dzina Lanu Ndinu Yehova” ndi Pemphelo
Cikumbutso: Lizani nyimbo yonse kamodzi, kenako mpingo uimbile pamodzi nyimbo yatsopanoyo.