Ndandanda ya Mlungu wa July 6
MLUNGU WA JULY 6
Nyimbo 80 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 12 ndime 1-8 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 1 Mafumu 7-8 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Mafumu 8:27-34 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Koneliyo—Mutu: Yehova Mulungu Alibe Tsankho—w14 9/15 tsa. 8 ndime 5-6 (Mph. 5)
Na. 3: Mungapilile Bwanji Nkhawa? —igw-CIN tsa. 24 ndime 1-3 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: “Kumbukilani masiku akale.”—Deut. 32:7.
Nyimbo 69
Mph. 10: Kugaŵila Magazini mu July. Kukambilana. Yambani ndi citsanzo coonetsa mmene mungagaŵile magazini pogwilitsila nchito maulaliki acitsanzo. Ndiyeno kambilanani maulaliki onse.
Mph. 10: Zosoŵa za pampingo.
Mph. 10: Tinacita Zotani? Kukambilana. Pemphani ofalitsa kuti afotokoze mmene apindulila pogwilitsila nchito mfundo za m’nkhani yakuti, “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuyambitsa Phunzilo la Baibulo Pogwilitsila Nchito Kabuku ka Uthenga Wabwino Wocokela Kwa Mulungu.” Pemphani omvela kuti afotokoze zocitika zosangalatsa za mu ulaliki.
Nyimbo 67 ndi Pemphelo