LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 11/15 tsa. 4
  • Maulaliki Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki Acitsanzo
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Nkhani Zofanana
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Maulaliki Acitsanzo
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2012
Onaninso Zina
Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
km 11/15 tsa. 4

Maulaliki Acitsanzo

Nsanja ya Mlonda November-December

“Anthu ambili sadziŵa kuti Baibulo lili ndi mayankho okhutilitsa a mafunso monga awa. [Muonetseni mafunso ali kuciyambi kwa nkhani yoyamba m’magazini a Nsanja ya Mlonda ndi kuŵelenga naye 2 Timoteyo 3:16.] Magazini iyi ifotokoza mmene mungapezele mayankho m’Baibulo lanu.”

Galamukani! December

“Masiku ano anthu ambili amapanikizika ndi mavuto? Kodi inunso mumaona conco? [Yembekezani ayankhe.] Baibulo limanena kuti tifunika kukhala ndi maganizo oyenela tikakumana ndi zovuta. [Ŵelengani Miyambo 24:10.] Magaziniyi ili ndi mfundo zotithandiza kuti tipilile ndipo ikufotokoza zitsanzo za anthu amene akupilila mavuto osiyanasiyana.”

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani