December 25-31
MALAKI 1-4
Nyimbo 131 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kodi Cikwati Canu Cimakondweletsa Yehova?”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Malaki.]
Mal. 2:13, 14—Yehova amadana ndi ocita cinyengo m’cikwati (jd peji 125-126 mapa. 4-5)
Mal. 2:15, 16—Khulupilikani kwa mnzanu wa m’cikwati (w02 5/1 peji 18 pala. 19)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mal. 1:10—N’cifukwa ciani tifunika kulambila Mulungu cifukwa comukonda ndiponso cifukwa cokonda anzathu? (w07 12/15 peji 27 pala. 1)
Mal. 3:1—Kodi vesi iyi inakwanilitsika bwanji m’nthawi za atumwi? Nanga masiku ano? (w13 7/15 peji 17 mapa. 5-6)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mal. 1:1-10
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) 1 Akor. 15:26—Phunzitsani Coonadi.
Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yes. 26:19; 2 Akor. 1:3, 4—(Onani mwb16.08 peji 8 pala. 2.)
Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) w07 12/15 peji 28 pala. 1—Mutu Wake: Kodi Timapeleka Bwanji Cakhumi ku Nyumba Yosungilamo Zinthu Masiku Ano?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Chikondi Chenicheni”: (15 min.) Mafunso na mayankho.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy nkhani 1
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 96 na Pemphelo