December Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano December 2017 Maulaliki a Citsanzo December 4-10 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | ZEFANIYA 1-HAGAI 2 Funani Yehova Tsiku la Mkwiyo Wake Lisanafike December 11-17 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | ZEKARIYA 1-8 “Adzagwila Covala ca Munthu Amene ndi Myuda” UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kunola Luso Lathu mu Ulaliki —Kufikila Munthu Aliyense m’Gawo Lathu December 18-24 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | ZEKARIYA 9-14 Khalani m’Cigwa ca “Pakati pa Mapili” UMOYO WATHU WACIKHRISTU Mbali Yatsopano pa Msonkhano wa Mkati mwa Wiki December 25-31 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALAKI 1-4 Kodi Cikwati Canu Cimakondweletsa Yehova? UMOYO WATHU WACIKHRISTU Chikondi Chenicheni