CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALAKI 1-4
Kodi Cikwati Canu Cimakondweletsa Yehova?
2:13-16
M’nthawi ya Malaki, Aisiraeli ambili anali kusudzulana pa zifukwa zopanda pake. Amene anali kucitila cinyengo anzawo a m’cikwati, kulambila kwawo kunali kosalandilika kwa Yehova
Yehova anadalitsa anthu olemekeza anzawo a m’cikwati
Kodi a m’cikwati angakhale bwanji okhulupilika . . .
m’maganizo?
pa zimene amaona?
m’zokamba zawo?