LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 July tsa. 5
  • “Ndinu Ofunika Kwambili Kuposa Mpheta Zambili”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Ndinu Ofunika Kwambili Kuposa Mpheta Zambili”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Tizikumbukila Kupemphelela Akhiristu Anzathu Amene Akuzunzidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Dzikolo ‘Linameza Mtsinje’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2022
  • Pitani Mukapange Ophunzila—Cifukwa ciani, Kuti, ndipo Motani?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 July tsa. 5

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | LUKA 12-13

“Ndinu Ofunika Kwambili Kuposa Mpheta Zambili”

12:6, 7

Mpheta ziŵili

Kodi Yesu anatanthauza ciani pokamba mau a pa Luka 12:6, 7? Mu vesi 4, timaŵelenga kuti Yesu anauza otsatila ake kuti asamaope anthu amene angawatsutse ngakhale amene angawaphe. Yesu anali kukonzekeletsa ophunzila ake za citsutso cimene iwo anali kudzayang’anizana naco m’tsogolo. Iye anawatsimikizila kuti Yehova amaona mtumiki wake aliyense kukhala wofunika, na kuti sadzalola kuti avutitsidwe kwamuyaya.

Tingatengele bwanji citsanzo ca Yehova pankhani yodela nkhawa anthu amene akuzunzidwa?

N’kuti kumene tingapeze nkhani yokhudza Mboni za Yehova zimene zili m’ndende palipano cifukwa ca cikhulupililo cawo?

Pali pano, abale na alongo ali m’ndende.

M’bale akupemphela m’ndende
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani