LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsa. 8
  • Tizikumbukila Kupemphelela Akhiristu Anzathu Amene Akuzunzidwa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tizikumbukila Kupemphelela Akhiristu Anzathu Amene Akuzunzidwa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Nkhani Zofanana
  • Nkhani Zodalilika Komanso Zolimbitsa Cikhulupililo
    Mmene Zopeleka Zanu Zimagwilila Nchito
  • Kondwelani Pamene Mukuzunzidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Musamaiwale Kupemphelela Anthu Ena
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
  • Pezani Nzelu Zothandiza pa Umoyo pa JW.ORG
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 January tsa. 8

UMOYO WACIKHIRISTU

Tizikumbukila Kupemphelela Akhiristu Anzathu Amene Akuzunzidwa

Baibo inakambilatu kuti Satana adzatizunza pofuna kulepheletsa utumiki wathu. (Yoh. 15:20; Chiv. 12:17) Kodi tingawathandize bwanji Akhiristu anzathu amene akuzunziwa m’maiko ena? Tiziwapemphelela. “Pembedzelo la munthu wolungama limagwila nchito mwamphamvu kwambili.”—Yak. 5:16.

M’bale ali mu unyolo amungenetsa mu jele; kagulu ka abale na alongo; m’bale apemphela

Kodi tingawapemphelele zinthu ziti? Tingapemphe Yehova kuti athandize abale na alongo athu kukhala olimba mtima ndi opanda mantha. (Yes. 41:10-13) Tingapemphelelenso olamulila kuti azitikomela mtima pa nchito yathu yolalikila, “kuti tikhale ndi moyo wabata ndi wamtendele.”—1 Tim. 2:1, 2.

Pamene Paulo na Petulo anali kuzunziwa, Akhiristu a m’nthawi yawo anali kuwapemphelela mocita kuwatomola maina. (Mac. 12:5; Aroma 15:30, 31) Ngakhale kuti sitingadziŵe maina onse a abale athu amene akuzunziwa, tingangotomola mpingo, dziko, kapena dela lakwawo.

  • Nkhani zatsopano zokhudza Mboni za Yehova zimene zikuzunziwa mungazipeze pa jw.org. (Yendani pa MALO A NKHANI > ZOKHUDZANA NDI MALAMULO.)

  • Nkhani ya pa jw.org yakuti, “Mayiko Amene a Mboni za Yehova Akumangidwa Chifukwa Chotsatira Zimene Amakhulupirira” ionetsa ziŵelengelo za Mboni zimene zili m’ndende m’maiko osiyana-siyana. (Yendani pa MALO A NKHANI > ZOKHUDZANA NDI MALAMULO.) Tinikani pa dziko lililonse kuti mudziŵe zambili, komanso kuti mupeze PDF yoonetsa maina a omangidwa kumeneko.

Nifuna nizipemphelelako Akhiristu anzathu amene akuzunziwa m’maiko aya:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani