LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsa. 6
  • October 22-28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 22-28
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 October tsa. 6

October 22-28

Yohane 15-17

  • Nyimbo 129 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Simuli Mbali ya Dzikoli”: (10 min.)

    • Yoh. 15:19—Otsatila a Yesu sali “mbali ya dzikoli” (“dzikoli” nwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 15:21—Otsatila a Yesu amazondewa cifukwa ca dzina lake (“cifukwa ca dzina langa” nwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 16:33—Otsatila a Yesu angagonjetse dziko ngati atengela citsanzo cake (it-1 peji 516)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yoh. 17:21-23—Kodi ophunzila a Yesu anali kudzakhala “amodzi” m’lingalilo lotani? (“amodzi” “akhale mu umodzi weni-weni” nwtsty mfundo zounikila)

    • Yoh. 17:24—Kodi “maziko a dziko” n’ciani? (“maziko a dziko” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 17:1-14

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba, ndipo gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 14 mapa. 3-4

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 101

  • “Akhristu Oona Amadziŵika na Cikondi—Kuteteza Mgwilizano Wathu Wapadela”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti “Muzikondana”—Musamasunge Zifukwa. Ngati nthawi ilola kambilanani kabokosi kakuti “Citsanzo ca m’Baibo Cofunika Kucisinkha-sinkha.”

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 40

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 106 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani