CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 15-17
“Simuli Mbali ya Dzikoli”
Yesu anagonjetsa dziko mwa kusatengela nzelu za dziko ngakhale pang’ono
Otsatila a Yesu afunika kukhala olimba mtima kuti asadetsedwe na makhalidwe kapena zocita za anthu owazungulila
Kusinkha-sinkha citsanzo ca Yesu, amene anagonjetsa dziko, kungatithandize kukhala olimba mtima potengela citsanzo cake