LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 10
  • Phindu la Nzelu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Phindu la Nzelu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Pemphelo la Solomo Lodzicepetsa Komanso Locokela Pansi pa Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Anagwila Nchito Molimbika Cifukwa Cokonda Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Tamandani Yehova Cifukwa ca Nzelu Zake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nzelu Yeniyeni Imafuula
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 10
Solomo akuweluza mlandu wa mahule aŵili amene akulimbilana mwana.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Phindu la Nzelu

Solomo anapempha nzelu kwa Yehova (1 Maf. 3:7-9; w11 12/15 8 ¶4-6)

Yehova anakondwela nalo pempho la Solomo (1 Maf. 3:10-13)

Cifukwa cakuti Solomo anali kuona nzelu zocokela kwa Mulungu kukhala zofunika, Aisiraeli anakhala pamtendele (1 Maf. 4:25)

Munthu wanzelu komanso womvetsa zinthu amaseŵenzetsa cidziŵitso cimene ali naco kuti cimuthandize kupanga zisankho zabwino. Nzelu ni yamtengo wapatali kuposa golide. (Miy. 16:16) Tingapeze nzelu mwa kuzipempha kwa Mulungu, kumuopa, kukhala odzicepetsa, na kuzifunafuna m’Mawu ake.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani