LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g20 na. 3 tsa. 16
  • Anagonjetsa Tsankho

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Anagonjetsa Tsankho
  • Galamuka!—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Onetsani Cikondi
    Galamuka!—2020
  • Thandizo Ilipo
    Galamuka!—2020
  • 12 Zolinga
    Galamuka!—2018
  • Thandizani Ana Anu Kukhala na Cikhulupililo Colimba mwa Mlengi Wawo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Galamuka!—2020
g20 na. 3 tsa. 16

Anagonjetsa Tsankho

Pitani pa jw.org kuti mumve za umoyo wa anthu awa na ena.

Abale eni-eni

Johny na Gideon akupatsa moni ana kunja kwa Nyumba ya Ufumu ya Mboni za Yehova.

Johny na Gideon anakhala mabwenzi apamtima olo kuti anali a mitundu yosiyana ndiponso anali na maganizo osiyana pandale.

Tambani vidiyo yakuti Johny na Gideon: Anali Adani, Tsopano ni Abale. Isakileni vidiyo imeneyi pa jw.org mwa kulemba mutu umenewu pa danga lofufuzila.

“N’nali Kufuna Kugwebana na Kupanda Cilungamo”

Rafika Morris.

Rafika analoŵa m’gulu la anthu ofuna kugwebana na khalidwe la kusankhana mitundu. Koma pamene anapezeka pa msonkhano wacigawo wa Mboni za Yehova, anapeza mgwilizano umene anali kufuna.

Tambani vidiyo yakuti Rafika Morris: N’nali Kufuna Kugwebana na Kupanda Cilungamo. Isakileni vidiyo imeneyi pa jw.org mwa kulemba mutu umenewu pa batani lofufuzila.

Anagonjetsa cidani

Zithunzi: 1. Muarabu akuyenda pamodzi na munthu wina ndipo akukambilana. 2. Myuda akumwetulila pamene ali na anzake.

N’ciani cinathandiza Mluya na Myuda wina kugonjetsa tsankho limene anali nalo?

Tambani vidiyo yakuti Kodi Cikondi Cidzagonjetsa Liti Cidani? Fufuzani vidiyo imeneyi pa jw.org mwa kulemba mutu umenewu pa batani lofufuzila.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani