LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 15
  • Zolengedwa Zimasonyeza Ulemerero wa Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zolengedwa Zimasonyeza Ulemerero wa Yehova
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Yendani ndi Mulungu!
    Imbirani Yehova
  • Mulungu Ayamba Kupanga Vinthu
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Zakumwamba Zilengeza Ulemelelo wa Mulungu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Zakumwamba Zimalengeza Ulemerero wa Mulungu
    Imbirani Yehova
Imbirani Yehova
sn nyimbo 15

Nyimbo 15

Zolengedwa Zimasonyeza Ulemerero wa Yehova

(Salmo 19)

1. Yehova inetu ndimadziwa

Zamlengalenga ndi zodabwitsa.

Zimalemekeza dzina lanu

Ngakhale sizitulutsa mawu.

Zimalemekeza dzina lanu

Ngakhale sizitulutsa mawu.

2. Munalenga nyenyezi ndi dzuwa,

Munaika malire a nyanja.

Munalenga zinthu zodabwitsa

Komabe mumatiganizira.

Munalenga zinthu zodabwitsa

Komabe mumatiganizira.

3. Malamulo anu ndi oyera

Ndipo moyo amabwezeretsa.

N’ngofunika kuposa golide,

Tiwasungedi tiwatsatire.

N’ngofunika kuposa golide,

Tiwasungedi tiwatsatire.

(Onaninso Sal. 12:6; 89:7; 144:3; Aroma 1:20.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani