LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 23
  • Yehova Ndiye Mphamvu Yathu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Ndiye Mphamvu Yathu
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Ndiye Mphamvu Yathu
    Imbirani Yehova
  • Mvelani Pemphelo Langa Conde
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Mulungu Imvani Pemphero Langa
    Imbirani Yehova
  • Funani Cipulumutso ca Mulungu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 23

Nyimbo 23

Yehova Ndiye Mphamvu Yathu

(Yesaya 12:2)

1. Yehova inu ndi mphamvu yathu.

Inu ndinu Mpulumutsi wathu.

Mboni zanufe timalalika.

Kaya ’nthu amve kaya akane.

(KOLASI)

Yehova, n’thanthwe ndi mphamvu yathu,

Tilengezabe Dzina lanu.

Yehova inu wamphamvu yonse,

Pobisala pathu, Nsanja yathu.

2. Tikondwa ndi kuunika kwanu;

Tatseguka m’maso ndi cho’nadi.

M’Malemba timvamo malamulo;

Ife tasankha Ufumu wanu.

(KOLASI)

Yehova, n’thanthwe ndi mphamvu yathu,

Tilengezabe Dzina lanu.

Yehova inu wamphamvu yonse,

Pobisala pathu, Nsanja yathu.

3. Tikutumikirani mokondwa,

Ngakhale Satana ’matinyoza.

Ngakhale atafuna kutipha,

Tikhalebe mbali ya Ufumu.

(KOLASI)

Yehova, n’thanthwe ndi mphamvu yathu,

Tilengezabe Dzina lanu.

Yehova inu wamphamvu yonse,

Pobisala pathu, Nsanja yathu.

(Onaninso 2 Sam. 22:3; Sal. 18:2; Yes. 43:12.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani