LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 126
  • Ntchito Imene Tagwira Chifukwa cha Chikondi

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ntchito Imene Tagwira Chifukwa cha Chikondi
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Nchito Yoonetsa Cikondi Cathu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Tikhala Monga mwa Dzina Lathu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Zochita Zathu Zizigwirizana ndi Dzina Lathu
    Imbirani Yehova
  • ‘Talaŵani, Muone Kuti Yehova ni Wabwino’
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 126

Nyimbo 126

Ntchito Imene Tagwira Chifukwa cha Chikondi

(Salimo 127:1)

1. Yehova tikufuna

Kupemphera mokhudzidwa.

Chifukwa mwatikonda ndipo

Tasangalala.

Taona mwadalitsa

Ntchito imene tagwira,

Ndipo tamangadi nyumbayi,

Mwatithandiza.

(KOLASI)

Kukumangirani nyumbayi

Yehova unali mwayi.

Nthawi zonse tilemekeze dzina lanu

Ndi kukutumikirani.

2. Mabwenzi okondwera,

Taonani tawapeza.

Sitidzaiwala mpakana

M’moyo wosatha.

Taona mzimu wanu

Mukugwirizana kwathu.

Mwayi taupeza wokwezadi

Dzina lanu.

(KOLASI)

Kukumangirani nyumbayi

Yehova unali mwayi.

Nthawi zonse tilemekeze dzina lanu

Ndi kukutumikirani.

(Onaninso Sal. 116:1; 147:1; Aroma 15:6.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani