LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 127
  • Mtundu wa Munthu Amene Niyenela Kukhala

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mtundu wa Munthu Amene Niyenela Kukhala
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Mtundu wa Munthu Amene Muyenera Kukhala
    Imbirani Yehova
  • Yehova Alangiza Mwacikondi Kuti: “Mwana Wanga, Khala Wanzelu”
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Yehova Akutipempha Mokoma Mtima Kuti: “Mwana Wanga, Khala Wanzeru”
    Imbirani Yehova
  • Ligwilitsileni Nchito Bwino Galasi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 127

NYIMBO 127

Mtundu wa Munthu Amene Niyenela Kukhala

Yopulinta

(2 Petulo 3:11)

  1. 1. Atate Yehova, ni mphatso yanji

    Ningakupatseni cifukwa ca moyo?

    Ndi Mau anu ine niphunzitseni;

    Nithandizeni kuona mtima wanga.

    (BILIJI)

    Ninadzipeleka na mtima wonse

    Kukutamandani moyo wanga wonse.

    Ninasankha ndekha kudzipeleka,

    Kukondweletsa imwe Yehova.

    Ine n’thandizeni kudziŵa mtundu

    wa munthu amene mufuna nikhale.

    Yehova ndinu wokhulupilikadi.

    Nidzakutumikilani kwa muyaya.

(Onaninso Sal. 18:25; 116:12; Miy. 11:20.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani