Musaleme pa Kucita Zabwino
KUM’MAŴA
8:30 Nyimbo
Zamalimba 8:40 Nyimbo Na. 77 na Pemphelo
8:50 N’cifukwa Ninji Kucita Zabwino Kumakhala Kovuta?
9:05 Yosiilana: Pewani Kufesela ku Thupi
Muziseŵenzetsa Mwanzelu ma Webusaiti a Maceza
Muzisankha Zosangalatsa Zabwino
Pewani Mzimu wa Kaduka
Konzani Tsogolo Lodalilika
10:05 Nyimbo Na. 45 na Zilengezo
10:15 Pitilizani Kucitila Onse Zabwino
10:30 Kudzipeleka na Ubatizo
11:00 Nyimbo Na. 63
KUMASANA
12:10 Nyimbo Zamalimba
12:20 Nyimbo Na. 127 na Pemphelo
12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Pewani Kuyesa Kupusitsa Mulungu—Motani?
13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:30 Nyimbo Na. 59 na Zilengezo
13:40 Yosiilana: Pitilizani Kufesela ku Mzimu
Kulitsani Cizoloŵezi Coŵelenga
Muzilola Mfundo za M’Baibo Kukutsogolelani
‘Dzanja Lanu Lisapumule’
14:40 Zimene Tidzatuta Tikapanda Kulema
15:15 Nyimbo Na. 126 na Pemphelo