Tsiku Laciŵili
“YENDANIBE M’CIKONDI”—AEFESO 5:2
KUM’MAŴA
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 85 na Pemphelo
8:40 YOSIILANA: Onetsani Cikondi Cosatha mu Mpingo
Kwa Amene Akutsogolela (1 Atesalonika 5:12, 13)
Kwa Akazi Amasiye ndi Ana Amasiye (Yakobo 1:27)
Kwa Okalamba (Levitiko 19:32)
Kwa Atumiki Anthawi Zonse (1 Atesalonika 1:3)
Kwa Alendo Ocokela ku Maiko Ena (Levitiko 19:34; Aroma 15:7)
9:50 Nyimbo Na. 58 na Zilengezo
10:00 YOSIILANA: Onetsani Cikondi Cosatha mu Ulaliki
Mwa Kuonetsa Cikondi Canu pa Mulungu (1 Yohane 5:3)
‘Uzikonda Mnansi Wako Mmene Udzikondela Wekha’ (Mateyu 22:39)
Muzikonda Mawu a Yehova (Salimo 119:97; Mateyu 13:52)
10:45 UBATIZO: Phunzilani Khalidwe la Cikondi kwa Yesu (Mateyu 11:28-30)
11:15 Nyimbo Na. 52 na Kupumula
KUMASANA
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 84
12:50 YOSIILANA: Mmene Abale Athu Amaonetsela Cikondi Cosatha . . .
mu Africa (Genesis 16:13)
ku Asia (Machitidwe 2:44)
ku Europe (Yohane 4:35)
ku North America (1 Akorinto 9:22)
ku Oceania (Salimo 35:18)
ku South America (Machitidwe 1:8)
13:55 YOSIILANA: Onetsani Cikondi Cosatha M’banja
Muzim’konda Mkazi Wanu (Aefeso 5:28, 29)
Muzim’konda Mwamuna Wanu (Aefeso 5:33; 1 Petulo 3:1-6)
Muziŵakonda Ana Anu (Tito 2:4)
14:35 Nyimbo Na. 35 na Zilengezo
14:45 FILIMU YAIKULU: Nkhani ya Yosiya: Kondani Yehova; Danani Naco Coipa—Gawo I (2 Mbiri 33:10-24; 34:1, 2)
15:15 Phunzitsani Ana Anu Kuonetsa Ena Cikondi (2 Timoteyo 3:14, 15)
15:50 Nyimbo Na. 134 na Pemphelo Lothela