Tsiku Lacitatu
“PITILIZANI KUCITA ZINTHU ZIMENE ZINGACITITSE MULUNGU KUKUKONDANI”—YUDA 21
KUM’MAŴA
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 106 na Pemphelo
8:40 YOSIILANA: Kumbukilani Mmene Cikondi Cilili
N’coleza Mtima Ndiponso N’cokoma Mtima (1 Akorinto 13:4)
Sicicita Nsanje; Sicidzitama (1 Akorinto 13:4)
Sicidzikuza; Sicicita Zosayenela (1 Akorinto 13:4, 5)
Sicisamala Zofuna Zake Zokha; Sicikwiya (1 Akorinto 13:5)
Sicisunga Zifukwa; Sicikondwela ndi Zosalungama (1 Akorinto 13:5, 6)
Cimakondwela ndi Coonadi; Cimakwilila Zinthu Zonse (1 Akorinto 13:6, 7)
Cimakhulupilila Zinthu Zonse; Cimayembekezela Zinthu Zonse (1 Akorinto 13:7)
Cimapilila Zinthu Zonse; Cikondi Sicitha (1 Akorinto 13:7, 8)
10:10 Nyimbo Na. 150 na Zilengezo
10:20 NKHANI YA ANTHU ONSE: Cikondi ca Zoona Cimapezeka M’dzikoli Lodzala Cidani—Koma Kuti? (Yohane 13:34, 35)
10:50 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
11:20 Nyimbo Na. 1 na Kupumula
KUMASANA
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 124
12:50 FILIMU YAIKULU: Nkhani ya Yosiya: Kondani Yehova; Danani Naco Coipa—Gawo II (2 Mafumu 22:3-20; 23:1-25; 2 Mbiri 34:3-33; 35:1-19)
13:20 Nyimbo ya mutu wakuti “Nilimbitseni Mtima” na Zilengezo
13:30 Ganizilani Nchito za Yehova Zoonetsa Cikondi Cake Cokhulupilika (Salimo 107:43; Aefeso 5:1, 2)
14:30 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela