‘Yembekezelani Yehova’ Mwacidwi!
SALIMO 130:6
M’mawa
08:30 Nyimbo Zamalimba
08:40 Nyimbo Na. 88 na Pemphelo
08:50 ‘Yembekezelani Yehova’ Mwacidwi—Motani?
09:05 Nkhani Yosiyilana: Tengelani Citsanzo ca Amene Anayembekezela Mwacidwi
• Habakuku
• Yohane
• Anna
10:05 Nyimbo Na. 142 na Zilengezo
10:15 Muyembekezela Ciyani?
10:30 Kudzipatulila na Ubatizo
11:00 Nyimbo Na. 28
Masana
12:10 Nyimbo Zamalimba
12:20 Nyimbo Na. 54 na Pemphelo
12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Kodi Kuleza Mtima N’kofunikabe?
13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:30 Nyimbo Na. 143 na Zilengezo
13:40 Nkhani Yosiyilana: Yembekezelani Yehova . . .
• Mukasungulumwa
• Mukalakwa
• Oipa Zinthu Zikamawayendela
14:40 “Wolungama Adzalandila Mphoto”
15:15 Nyimbo Na. 140 na Pemphelo