LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsa. 4
  • Umoyo Wabwino Koposa (The Best Life Ever)

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Umoyo Wabwino Koposa (The Best Life Ever)
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulila? (Mbali 1)
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Kufotokoza Zimene Timakhulupilila Zokhudza 1914
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Thandizo Ilipo
    Galamuka!—2020
  • Pemphani Thandizo Kuti Mumvetsetse Baibulo
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2016
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 February tsa. 4

UMOYO WATHU WACIKRISTU

Umoyo Wabwino Koposa (The Best Life Ever)

Acinyamata amene ali m’gulu la Yehova, ali ndi mipata yambili yotumikila Yehova. Onelelani vidiyo ya mutu wakuti Umoyo Wabwino Koposa (The Best Life Ever) kuti muone mmene Cameron anagwilitsila nchito nthawi yake mwanzelu monga wacinyamata. Kenako yankhani mafunso otsatilawa. (Pitani pa jw.org, ndi kuona pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > TEENAGERS.)

Cameron akuika cizindikilo pa mapu coonetsa mtunda kucokela ku United States mpaka ku Malawi
  • Ndi nchito iti imene Cameron amakonda kwambili kucita?

  • Ndi liti pamene anaganiza zoonjezela utumiki wake? Nanga anacita liti zimenezo?

  • N’ciani cinamuthandiza kukonzekela kukatumikila ku dela limene kuli ofalitsa ocepa m’dziko lina?

    Cameron aŵelengela lemba mai wina ku Malawi
  • Ndi mavuto otani amene Cameron anakumana nao pamene anali kutumikila m’dziko lina?

  • N’cifukwa ciani n’zopindulitsa kutumikila Yehova ku dela lacilendo?

  • Ndi madalitso otani amene Cameron anakhala nao?

    Abale ndi alongo ku Malawi akubaibisa
  • N’cifukwa ciani kutumikila Yehova ndiye umoyo wabwino koposa?

  • Ndi mipata ina iti imene acinyamata ali nayo m’gulu la Yehova?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani