CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | SALIMO 19-25
Maulosi Amatiuza Zambili Zokhudza Mesiya
LEMBA |
ULOSI |
KUKWANILITSIDWA KWAKE |
---|---|---|
Salimo 22:1 |
Anaoneka ngati wasiidwa ndi Mulungu |
|
Salimo 22:7, 8 |
Ananyozedwa ali pa mtengo wozunzikilapo |
|
Salimo 22:16 |
Anakhomeleledwa ndi misomali pa mtengo wozunzikilapo |
|
Salimo 22:18 |
Kucita maele pa zovala zake |
|
Salimo 22:22 |
Amatsogolela panchito yodziŵitsa anthu za dzina la Yehova |