LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsa. 6
  • Maphunzilo Aumulungu Amagonjetsa Tsankho

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maphunzilo Aumulungu Amagonjetsa Tsankho
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Tsankho—Kodi Na Imwe Muli Nalo?
    Galamuka!—2020
  • Tikhale Amodzi, Monga Mmene Yehova na Yesu Alili Amodzi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Anagonjetsa Tsankho
    Galamuka!—2020
  • Onetsani Cikondi
    Galamuka!—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 December tsa. 6

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

Maphunzilo Aumulungu Amagonjetsa Tsankho

Yehova alibe tsankho. (Mac. 10:34, 35) Iye amalandila munthu aliyense wocokela “m’dziko lililonse, fuko lililonse, mtundu uliwonse ndi cinenelo ciliconse.” (Chiv. 7:9) Conco, mumpingo wacikhiristu mulibe malo a tsankho. (Yak. 2:1-4) Timayamikila maphunzilo aumulungu, ndipo timakondwela na paradaiso wauzimu amene wathandiza kuti anthu asinthe maumunthu awo. (Yes. 11:6-9) Pamene ticita zonse zotheka kuchotsa tsankho iliyonse mumtima mwathu, timatengela Mulungu.—Aef. 5:1, 2.

Johny na Gideon alandila ana pa Nyumba ya Ufumu

TAMBANI VIDIYO YAKUTI JOHNY NA GIDEON: ANALI ADANI, TSOPANO NI ABALE. NDIYENO YANKHANI MAFUNSO OTSATILA:

  • N’cifukwa ciani maphunzilo aumulungu amapambana zimene athu ayesa kucita kuti acotsepo tsankho?

  • N’ciani cimakukondweletsani ndi ubale wathu wa padziko lonse?

  • Kodi Yehova amalemekezeka bwanji tikapitiliza kukhala Akhiristu ogwilizana?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani